Psalms 63:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzandikhutitsa ndi zonona, ndipo ndidzakutamandani ndi mau osangalala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzakhutitsa moyo wanga ngati ndi mafuta ndi chonona; ndipo pakamwa panga ndidzakulemekezani ndi milomo yakufuula mokondwera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzakhutitsa moyo wanga ndi zonona. Ine ndidzakutamandani ndi mawu anthetemya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzakhutitsa moyo wanga ngati ndi mafuta ndi zonona; Ndipo pakamwa panga ndidzakulemekezani ndi milomo yakupfuula mokondwera;