Psalms 63:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikagona pabedi panga ndimalingalira za Inu, usiku wonse ndimasinkhasinkha za Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pokumbukira Inu pa kama wanga, ndi kulingalira za Inu maulonda a usiku.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa bedi panga ndimakumbukira inu; ndimaganiza za Inu nthawi yonse ya usiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pokumbukira Inu pa kama wanga, Ndi kulingalira za Inu maulonda a usiku.