Psalms 63:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mwakhala chithandizo changa, motero ndikuimba ndi chimwemwe pansi pa mapiko anu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti munakhala mthandizi wanga; ndipo ndidzafuula mokondwera mu mthunzi wa mapiko anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa ndinu thandizo langa, ine ndimayimba mu mthunzi wa mapiko anu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti munakhala mthandizi wanga; Ndipo ndidzapfuula mokondwera mu mthunzi wa mapiko anu.