Psalms 63:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wanga ukukangamira Inu, dzanja lanu lamanja likundichirikiza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Moyo wanga uumirira Inu. Dzanja lamanja lanu lindigwiriziza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Moyo wanga umakangamira Inu; dzanja lanu lamanja limandigwiriziza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Moyo wanga uumirira Inu: Dzanja lamanja lanu lindigwiriziza.