Psalms 63:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu amene amayesayesa kuwononga moyo wanga, adzatsikira ku dziko la anthu akufa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma iwo amene afuna moyo wanga kuti auononge, adzalowa m'munsi mwake mwa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amene akufunafuna moyo wanga adzawonongedwa; adzatsikira kunsi kozama kwa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma iwo amene afuna moyo wanga kuti auononge, Adzalowa m'munsi mwace mwa dziko.