Psalms 64:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Imvani mau anga, Inu Mulungu, pamene ndikukudandaulirani. Tetezani moyo wanga kwa mdani woopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide. Imvani Yehova, mau anga, m'kudandaula kwanga; sungani moyo wanga angandiopse mdani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. Ndimvereni Mulungu pomwe ndikunena madandawulo anga; tetezani moyo wanga ku chiopsezo cha mdani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Imvani Yehova, mau anga, m'kudandaula kwanga; Sungani moyo wanga angandiopse mdani.