Psalms 64:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adalitse anthu ake mtendere ndi chimwemwe zikhale nao, anthu akondwere chifukwa cha Chauta
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wolungama adzakondwera mwa Yehova, nadzakhulupirira Iye; ndipo oongoka mtima onse adzalemekeza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Lolani wolungama akondwere mwa Yehova ndi kubisala mwa Iye, owongoka mtima onse atamande Iye!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wolungama adzakondwera mwa Yehova, nadzakhulupirira Iye; Ndipo oongoka mtima onse adzalemekeza.