Psalms 64:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tchinjirizeni ku upo wachiwembu wa anthu oipa, tetezeni ku chiwawa cha anthu ochita zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndibiseni pa upo wachinsinsi wa ochita zoipa; pa phokoso la ochita zopanda pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndibiseni ku chiwembu cha anthu oyipa, ku gulu laphokoso la anthu ochita zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndibiseni pa upo wacinsinsi wa ocita zoipa; Pa phokoso la ocita zopanda pace: