Psalms 64:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo amanola lilime lao ngati lupanga, amaponya mau obaya ngati mivi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene anola lilime lao ngati lupanga, napiringidza mivi yao, ndiyo mau akuwawitsa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amanola malilime awo ngati malupanga, amaponya mawu awo olasa ngati mivi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene anola lilime lao ngati lupanga, Napiringidza mibvi yao, ndiyo mau akuwawitsa;