Psalms 64:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amabisalira anthu osalakwa namaŵalasa modzidzimutsa ndi mopanda mantha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuponyera wangwiro mobisika: Amponyera modzidzimutsa, osaopa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amaponya mivi yawo ali pa malo wobisala kwa munthu wosalakwa; amamulasa modzidzimutsa ndi mopanda mantha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuponyera wangwiro mobisika: Amponyera modzidzimutsa, osaopa.