Psalms 64:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Amaganizira zoipa nkumati, “Takonza mochenjera ndithu chiwembu chathu.” Malingaliro ndi zofuna za mtima wa munthu nzobisika.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Afunafuna zosalungama; kusanthula, asanthuladi mpaka kutha; chingakhale cha m'kati mwake mwa munthu, ndi mtima wozama.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo amakonzekera zosalungama ndipo amati, “Takonza ndondomeko yabwino kwambiri!” Ndithu maganizo ndi mtima wa munthu ndi zachinyengo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Afunafuna zosalungama; kusanthula, asanthuladi kutha; Cingakhale ca m'kati mwace mwa munthu, ndi mtima wozama.