Psalms 64:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pompo anthu onse adzachita mantha, adzasimba zimene Mulungu wachita, adzalingalira zomwe Mulungu wachitazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anthu onse adzachita mantha; nadzabukitsa chochita Mulungu, nadzasamalira ntchito yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu onse adzachita mantha; adzalengeza ntchito za Mulungu ndi kulingalira mozama zomwe Iye wazichita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anthu onse adzacita mantha; Nadzabukitsa cocita Mulungu, Nadzasamalira nchito yace.