Psalms 65:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, anthu azikutamandani ku Ziyoni, achitedi zimene adalumbira kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo; Salimo la Davide. Nyimbo. M'Ziyoni akulemekezani Inu mwachete, Mulungu, adzakuchitirani Inu chowindachi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. Nyimbo. Matamando akudikira Inu Mulungu mu Ziyoni; kwa inu malumbiro athu adzakwaniritsidwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
M'Ziyoni akulemekezani Inu mwacete, Mulungu: Adzakucitirani Inu cowindaci.