Psalms 65:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
chifukwa cha machimo ao. Pamene zochimwa zathu zitipambana, Inu mumazifafaniza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mphulupulu zinandilaka; koma mudzafafaniza zolakwa zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene tinathedwa nzeru ndi machimo, Inu munakhululukira mphulupulu zathu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mphulupulu zinandilaka; Koma mudzafafaniza zolakwa zathu.