Psalms 65:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mumachititsa bata mkokomo wa nyanja ndi mkokomo wa mafunde ndi phokoso la mitundu ina ya anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amene atontholetsa kukuntha kwa nyanja, kukuntha kwa mafunde ake, ndi phokoso la mitundu ya anthu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amene munakhalitsa bata nyanja kukokoma kwa mafunde ake, ndi phokoso la anthu a mitundu ina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amene atontholetsa kukuntha kwa nyanja, kukuntha kwa mafunde ace, Ndi phokoso la mitundu ya anthu.