Psalms 66:1 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tamandani Mulungu ndi chimwemwe mokweza mau, inu anthu onse a pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo. Nyimbo, Salimo. Fuulirani kwa Mulungu, dziko lonse lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo. Fuwulani kwa Mulungu ndi chimwemwe, dziko lonse lapansi!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pfuulirani kwa Mulungu, dziko lonse lapansi.