Psalms 66:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudalola kuti adani atikwere pa mutu, tidaloŵa m'moto ndiponso m'madzi, komabe Inu mwatifikitsa ku malo opulumukirako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munapititsa anthu oberekeka pamwamba pamitu pathu; tinapyola moto ndi madzi; koma munatifikitsa potitsitsimutsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munalola kuti anthu akwere pa mitu yathu; ife tinadutsa mʼmoto ndi mʼmadzi, koma Inu munatibweretsa ku malo a zinthu zochuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munapititsa anthu oberekeka pamwamba pamitu pathu; Tinapyola moto ndi madzi; Koma munatifikitsa potitsitsimutsa.