Psalms 66:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
zimene ndidalankhula ndi pakamwa panga, ndiponso zimene ndidalonjeza pamene ndinali pa mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
zimene inazitchula milomo yanga, ndinazinena pakamwa panga posautsika ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malumbiro amene milomo yanga inalonjeza ndi pakamwa panga panayankhula pamene ndinali pa mavuto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zimene inazichula milomo yanga, Ndinazinena pakamwa panga pasautsika ine.