Psalms 66:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muuzeni Mulungu kuti, “Ntchito zanu nzodabwitsa kwambiri. Mphamvu zanu nzazikulu, kotero kuti adani anu amakuŵeramirani moopa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nenani kwa Mulungu, Ha, ntchito zanu nzoopsa nanga! Chifukwa cha mphamvu yanu yaikulu adani anu adzagonjera Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nenani kwa Mulungu, “Ntchito zanu ndi zoopsa ndithu! Mphamvu yanu ndi yayikulu kwambiri kotero kuti adani anu amawerama pamaso panu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nenani kwa Mulungu, Ha, nchito zanu nzoopsa nanga! Cifukwa ca mphamvu yanu yaikuru adani anu adzagonjera Inu,