Psalms 66:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Bwerani mudzaone zimene Mulungu wachita, ntchito zake nzodabwitsa pakati pa anthu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Idzani, muone ntchito za Mulungu; zochitira Iye ana a anthu nzoopsa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwerani mudzaone zimene Mulungu wachita, ntchito zanu ndi zoopsa ndithu pakati pa anthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Idzani, muone nchito za Mulungu; Zocitira Iye ana a anthu nzoopsa.