Psalms 66:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adasandutsa nyanja kuti ikhale nthaka youma. Anthu adaoloka mtsinje uja poyenda pansi. Nchifukwa chake timukondwerere Iye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anasanduliza nyanja ikhale mtunda. Anaoloka mtsinje choponda pansi, apo tinakondwera mwa Iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anasandutsa nyanja kukhala malo owuma, iwo anawoloka pa madzi ndi mapazi. Bwerani, tiyeni tikondwere mwa Iye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anasanduliza nyanja ikhale mtunda: Anaoloka mtsinje coponda pansi: Apo tinakondwera mwa Iye.