Psalms 67:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mitundu ya anthu isangalale ndi kuimba ndi chimwemwe, chifukwa Inu mumaweruza anthu mwachilungamo, ndi kuŵatsogolera pa dziko lapansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Anthu akondwere, nafuule mokondwera; pakuti mudzaweruza anthu molunjika, ndipo mudzalangiza anthu pa dziko lapansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mitundu yonse ya anthu isangalale ndi kuyimba mwachimwemwe, pakuti inu mumaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo ndi kutsogolera mitundu ya anthu a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Anthu akondwere, napfuule makondwera; Pakuti mudzaweruza anthu malunjika, Ndipo mudzalangiza anthu pa dziko lapansi.