Psalms 68:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adzambatuke, adani ake amwazikane. Onse amene amamuda, athaŵe pamaso pake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Mkulu wa Nyimbo. Salimo la Davide. Nyimbo. Auke Mulungu, abalalike adani ake; iwonso akumuda athawe pamaso pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa mtsogoleri wa mayimbidwe. Salimo la Davide. Adzuke Mulungu, adani ake amwazikane; adani ake athawe pamaso pake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Auke Mulungu, abalalike adani ace; Iwonso akumuda athawe pamaso pace.