Psalms 68:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu anu adapezamo malo okhala. Inu Mulungu, mudapatsa anthu osauka zosoŵa zao mwa ubwino wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Gulu lanu linakhala m'dziko muja. Mwa ukoma wanu munalikonzera ozunzika, Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu anu anakhala mʼmenemo ndipo munapatsa anthu osauka zimene zinkawasowa chifukwa cha ubwino wanu Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Gulu lanu linakhala m'dziko muja: Mwa ukoma wanu munalikonzera ozunzika, Mulungu.