Psalms 68:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Zofunkhazo zikuwoneka ngati mapiko a nkhunda okutidwa ndi siliva, nthenga zake nzokutidwa ndi golide wonyezemira.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pogona inu m'makola a zoweta, mukhala ngati mapiko a njiwa okulira ndi siliva, ndi nthenga zake zokulira ndi golide woyenga wonyezimira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngakhale mukugona pakati pa makola a ziweto, mapiko a nkhunda akutidwa ndi siliva, nthenga zake ndi golide wonyezimira.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pogona inu m'makola a zoweta, Mukhala ngati mapiko a njiwa okulira ndi siliva, Ndi nthenga zace zokulira ndi golidi woyenga wonyezimira.