Psalms 68:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Mphambe adabalalitsa mafumu kumeneko, ku Zalimoni kudagwa chisanu choopsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Wamphamvuyonse anabalalitsa mafumu m'dzikomo, munayera ngati matalala m'Zalimoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Wamphamvuzonse anabalalitsa mafumu mʼdziko, zinali ngati matalala akugwa pa Zalimoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Wamphamvuyonse anabalalitsa mafumu m'dzikomo, Munayera ngati matalala m'Salimoni.