Psalms 68:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudakwera kumwamba, mutatenga am'ndende ambiri, ndipo mudalandira mphatso kwa anthu, ngakhale kwa anthu oukira, kuti mudzakhale kumeneko, Inu Chauta Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munakwera kunka kumwamba, munapita nao undende kuuyesa ndende; munalandira zaufulu mwa anthu, ngakhale mwa opikisana nanu, kuti Yehova Mulungu akakhale nao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Inu munakwera mmwamba, munatsogolera a mʼndende ambiri; munalandira mphatso kuchokera kwa anthu, ngakhale kuchokera kwa owukira, kuti Inu Mulungu, mukhale kumeneko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munakwera kumka kumwamba, munapita nao undende kuuyesa ndende; Munalandira zaufulu mwa anthu, Ngakhale mwa opikisana nanu, kuti Yehova Mulungu akakhale nao.