Psalms 68:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Mulungu adzatswanya mitu ya adani ake, mitu ya anthu onse oyenda m'machimo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Indedi Mulungu adzaphwanya mutu wa adani ake, pakati pa mutu pa iye woyendabe m'kutsutsika kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndithu Mulungu adzaphwanya mitu ya adani ake, zipewa za ubweya za iwo amene amapitiriza kuchita machimo awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Indedi Mulungu adzaphwanya mutu wa adani ace, Pakati pa mutu pa iye woyendabe m'kutsutsika kwace.