Psalms 68:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ambuye adati, “Ndidzaŵabweza adani anu kuchokera ku Basani, ndidzaŵabweza kuchokera ku nyanja yozama,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ambuye anati, Ndidzawatenganso ku Basani, ndidzawatenganso kozama kwa nyanja,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ambuye akunena kuti, “Ndidzawabweretsa kuchokera ku Basani; ndidzawabweretsa kuchokera ku nyanja zozama.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ambuye anati, Ndidzawatenganso ku Basana, Ndidzawatenganso kozama kwa nyanja: