Psalms 68:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kuti musambe mapazi anu m'magazi, kuti agalu anu anyambiteko magazi a adaniwo.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti uviike phazi lako m'mwazi, kuti malilime a agalu ako alaweko adani ako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kuti muviyike mapazi anu mʼmagazi a adani anu, pamene malilime a agalu anu akudyapo gawo lawo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kuti ubviike phazi lako m'mwazi, Kuti malilime a agaru ako alaweko adani ako.