Psalms 68:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patsogolo pao pali Benjamini mng'ono wa onsewo, akalonga a Yuda ali pambuyo, ndiponso akalonga a Zebuloni ndi akalonga a Nafutali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Apo pali Benjamini wamng'ono, wakuwachita ufumu, akulu a Yuda, ndi a upo wao, akulu a Zebuloni, akulu a Nafutali.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pali fuko lalingʼono la Benjamini, kuwatsogolera, pali gulu lalikulu la ana a mafumu a Yuda, ndiponso pali ana a mafumu a Zebuloni ndi Nafutali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Apo pali Benjamini wamng'ono, wakuwacita ufumu, Akuru a Yuda, ndi a upo wao, Akulu a Zebuloni, akulu a Naftali.