Psalms 68:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha Nyumba yanu ya ku Yerusalemu, mafumu amabwera ndi mphatso kwa Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa cha Kachisi wanu wa m'Yerusalemu mafumu adzabwera nacho chaufulu kukupatsani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa cha Nyumba yanu ku Yerusalemu, mafumu adzabweretsa kwa Inu mphatso.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa ca Kacisi wanu wa m'Yerusalemu Mafumu adzabwera naco caufulu kukupatsani.