Psalms 68:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma anthu anu Mulungu, akondwere, asangalale pamaso panu, inde, asekere ndi chimwemwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma olungama akondwere; atumphe ndi chimwemwe pamaso pa Mulungu; ndipo asekere nacho chikondwerero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma olungama asangalale ndi kukondwera pamaso pa Mulungu; iwo akondwere ndi kusangalala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma olungama akondwere; atumphe ndi cimwemwe pamaso pa Mulungu; Ndipo asekere naco cikondwerero.