Psalms 68:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Akazembe adzabwera kuchokera ku Ejipito. A ku Etiopiya adzafulumira kugonjera Mulungu pokweza manja ao kwa Iye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Akulu adzafumira ku Ejipito; Kusi adzafulumira kutambalitsa manja ake kwa Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nthumwi zidzachokera ku Igupto; Kusi adzadzipereka yekha kwa Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Akulu adzafumira ku Aigupto; Kushi adzafulumira kutambalitsa manja ace kwa Mulungu.