Psalms 68:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta amene amayenda mu mlengalenga, mlengalenga wakalekale. Imvani liwu lake, liwu lake lamphamvu zedi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Iye wakuberekeka pamwambamwamba, oyambira kale lomwe; taonani; amveketsa liu lake, ndilo liu lamphamvu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa Iye amene amakwera pa mitambo yakalekale ya mmwamba amene amabangula ndi mawu amphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwa Iye wakuberekeka pamwambamwamba, oyambira kale lomwe; Taonani; amveketsa liu lace, ndilo liu lamphamvu.