Psalms 68:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu osiyidwa, Mulungu amaŵapatsa malo okhalamo, am'ndende amaŵatulutsa kuti akhale pa ufulu, koma anthu oukira, amaŵapirikitsira ku nthaka yoguga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu amangitsira banja anthu a pa okha; atulutsa am'ndende alemerere; koma opikisana naye akhala m'dziko lopanda madzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu amakhazikitsa mtima pansi osungulumwa mʼmabanja, amatsogolera amʼndende ndi kuyimba; koma anthu osamvera amakhala ku malo owuma a dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu amangitsira banjaanthu a pa okha; Aturutsa am'ndende alemerere; Koma opikisana naye akhala m'dziko lopanda madzi.