Psalms 68:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, pamene munkatsogolera anthu anu, pamene munkayenda m'chipululu muja,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakutuluka paja, Inu Mulungu, ndi kutsogolera anthu anu, pakuyenda paja Inu m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene munatuluka kutsogolera anthu anu, Inu Mulungu, pamene munayenda kudutsa chipululu,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuturuka paja, Inu Mulungu, ndi kutsogolera anthu anu, Pakuyenda paja Inu m'cipululu;