Psalms 68:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, mudagwetsa mvula yokwanira pa dziko. Mudalimbitsanso dziko, choloŵa cha anthu anu, pamene lidaali lofooka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu, Mulungu, munavumbitsa chimvula, munatsitsimutsa cholowa chanu pamene chidathodwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munapereka mivumbi yochuluka, Inu Mulungu; munatsitsimutsa cholowa chanu cholefuka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu, Mulungu, munabvumbitsa cimvula, Munatsitsimutsa colowa canu pamene cidathodwa.