Psalms 69:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndidadzilanga posala zakudya, anthu adandinyoza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinalira pa kusala kwa moyo wanga, koma uku kunandikhalira chotonza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene ndikulira ndi kusala kudya, ndiyenera kupirira kunyozedwa;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinalira pa kusala kwa moyo wanga, Koma uku kunandikhalira cotonza.