Psalms 69:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene ndidavala chiguduli kuwonetsa chisoni, ndidasanduka chinthu choŵaseketsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chovala changa ndinayesa chiguduli, koma amandiphera mwambi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
pomwe ndavala chiguduli, anthu amandiseweretsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo cobvala canga ndinayesa ciguduli, Koma amandiphera mwambi.