Psalms 69:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mundiyankhe, Inu Chauta, pakuti chikondi chanu chosasinthika nchabwino. Munditchere khutu chifukwa cha chifundo chanu chachikulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mundiyankhe Yehova; pakuti chifundo chanu nchokoma; munditembenukire monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiyankheni Inu Yehova mwa ubwino wanu wa chikondi chanu; mwa chifundo chanu chachikulu tembenukirani kwa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mundiyankhe Yehova; pakuti cifundo canu ncokoma; Munditembenukire monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanu.