Psalms 69:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Senderani pafupi, mundiwombole, mundipulumutse kwa adani anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yandikizani moyo wanga, ndi kuuombola; ndipulumutseni chifukwa cha adani anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Bwerani pafupi ndi kundilanditsa; ndiwomboleni chifukwa cha adani anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yandikizani moyo wanga, ndi kuuombola; Ndipulumutseni cifukwa ca adani anga,