Psalms 69:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adandipatsa ulembe kuti ndidye, ndipo nditamva ludzu, adandipatsa vinyo wosasa kuti ndimwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anandipatsa ndulu ikhale chakudya changa; nandimwetsa vinyo wosasa pomva ludzu ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayika ndulu mʼchakudya changa ndi kundipatsa vinyo wosasa chifukwa cha ludzu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anandipatsa ndulu ikhale cakudya canga; Nandimwetsa vinyo wosasa pomva ludzu ine.