Psalms 69:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muŵagwetsere ukali wanu, mkwiyo wanu woyaka moto uŵagwire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muwatsanulire mkwiyo wanu, ndipo moto wa ukali wanu uwagwere.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Khuthulirani ukali wanu pa iwo; mkwiyo wanu woyaka moto uwathe mphamvu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muwatsanulire mkwiyo wanu, Ndipo moto wa ukali wanu uwagwere.