Psalms 69:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo amazunza amene Inu mwamkantha, ndipo amene Inu mwamupweteka, iwo amaonjezera kumuvutitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti alondola amene Inu munampanda; ndipo akambirana za zowawa zao za iwo amene munawalasa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti iwo amazunza amene inu munamuvulaza ndi kuyankhula zowawa kwa amene munawapweteka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti alondola amene Inu munampanda; Ndipo akambirana za zowawa zao za iwo amene munawalasa.