Psalms 69:29 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma ine ndazunzika ndipo ndikumva kuŵaŵa. Nyamuleni Inu Mulungu, kuti ndipulumuke.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ine ndine wozunzika ndi womva zowawa; chipulumutso chanu, Mulungu, chindikweze pamsanje.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikumva zowawa ndi kuzunzika; lolani chipulumutso chanu, Inu Mulungu, chinditeteze.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ine ndine wozunzika ndi womva zowawa; Cipulumutso canu, Mulungu, cindikweze pamsanje.