Psalms 69:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndafooka ndi kulira kwanga, kum'mero kwanga kwauma. M'maso mwada pamene ndikuyembekezera Mulungu wanga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndalema ndi kufuula kwanga; kum'mero kwauma gwa! M'maso mwanga mwada poyembekeza Mulungu wanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndafowoka ndikupempha chithandizo; kummero kwanga kwawuma gwaa, mʼmaso mwanga mwada kuyembekezera Mulungu wanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndalema ndi kupfuula kwanga; kum'mero kwauma gwa: M'maso mwanga mwada poyembekeza Mulungu wanga.