Psalms 69:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ozunzika aone zimenezo ndipo asangalale, inu amene mumafunafuna Mulungu, mulimbenso mtima.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ofatsa anachiona, nakondwera, ndipo inu, ofuna Mulungu, mtima wanu ukhale ndi moyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wosauka adzaona ndipo adzasangalala, Inu amene mumafunafuna Mulungu, mitima yanu ikhale ndi moyo!
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ofatsa anaciona, nakondwera: Ndipo inu, ofuna Mulungu, mtima wanu ukhale ndi moyo.