Psalms 69:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu Mulungu, mumadziŵa kupusa kwanga, zolakwa zanga sizili zobisika pamaso panu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukudziwa uchitsiru wanga, Inu Mulungu, kulakwa kwanga sikuli kobisika kwa Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu, mudziwa kupusa kwanga; Ndipo kutsutsika kwanga sikubisikira Inu.