Psalms 69:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pakuti ndanyozedwa, nkhope yanga yagwidwa ndi manyazi chifukwa cha Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndalola chotonza chifukwa cha Inu, chimpepulo chakuta nkhope yanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti ndimapirira kunyozedwa chifukwa cha Inu, ndipo manyazi amaphimba nkhope yanga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndalola cotonza cifukwa ca Inu: Cimpepulo cakuta nkhope yanga,